Poetry Association of Malawi

Poetry Association of Malawi PAM brings together persons involved in the promotion of poetry in the country; to preserve Malawian culture through poetry; and edu-entertain the public.

Poetry Association of Malawi (PAM) was founded in 1997 when a group of poets met at Kamuzu Stadium upper ground among whom were Mr. Laurent Namarakha, late Aubrey Nazombe, Edward Chitseko and late George Chiingeni. PAM was registered on 4th September, 1998 by the Registrar General under the Trustees Incorporation Act of 1962. The Poetry Association of Malawi has the responsibility of ensuring the development and growth of the poetry industry in Malawi. It also ensures that the rights and welfare of the poets are protected. It was established under the Trustees Incorporation Act of 1962 in order to accomplish among others the following objectives:
• To bring together persons and/or groups involved in the promotion of poetry in the country;
• To promote and preserve Malawian culture through poetry; and
• To educate, inform and entertain the nation through poetic works.

13/09/2026

Mawu omwe tinganene kwa Copyright Fund ndi Zikomo!

Koma Copyright Fund yawalitsa tsogolo lathuyi ndi chani? Iri ndithumbatu lomwe amapereka ndalama kwa anthu, mabungwe kay...
12/09/2026

Koma Copyright Fund yawalitsa tsogolo lathuyi ndi chani? Iri ndithumbatu lomwe amapereka ndalama kwa anthu, mabungwe kaya nthambi zaboma zomwe zimagwira ntchito zaluso kapena zokhuzana ndi luso. Utha kukhala ndiwe mlakatuli,oyimba, kaya wazisuzo ndi ena ambiri, ngati uli ndi project yomwe itha kupititsa patsogolo industry ya zaluso, awa amapereka ndalama kuthandizira izi. Iwowa samangoperekatu ngati mana, umalemba propozo kufotokoza za malingaliro a project yako motsatira ndondomeko zomwe anazikonza iwowo. Akakaona kuti propozo yako ikugwirizana ndi zolinga zathumbazo basitu amakupatsa ndalama. Iwo akhala akutulutsanso call ina posachedwa. Tafufuzani zambiri mupindule.

Achina Copyright Fund abwera kudzatithandiza shuwa!

Nde anenano kuti chani apule pano tsopano pamene mpandawu watha?Iwo ati "Zikomo Kwambiri Copyright Fund pothandiza malot...
11/09/2026

Nde anenano kuti chani apule pano tsopano pamene mpandawu watha?

Iwo ati "Zikomo Kwambiri Copyright Fund pothandiza maloto athu. Tsiku lina tikamakadzalowa ku ma ofesi kwathu komwe kumanga mpanda kwake mwatithandiza sitizakuyiwalani. Apa mwawalitsa tsogolo la alakatuli ambiri!

Tawonga Copyright Fund.

Anati bwanji apule a Poetry Association of Malawi zitadziwika kuti Poetry Association yapeza mwayi wa ndalama zankhanink...
10/09/2026

Anati bwanji apule a Poetry Association of Malawi zitadziwika kuti Poetry Association yapeza mwayi wa ndalama zankhaninkhani zoti imangire mpanda pa Plot yawo ya ku Lilongwe?

Iwo anati! "M'malo mwa utsogoleri wa Poetry Association of Malawi, ndife othokoza Copyright Fund potsogolera ulendo wathu ofuna kukhala ndi ma ofesi. Mpanda omwe timange ndi ndalama zimenezi uthandiza kuti anthu asalowelere pa plot yathu komanso kupereka confidence kwa ena omwe angafune kutithandiza. Zikomo zikomo Copyright Fund!"

09/09/2026

Chikhulupiliro Chama Afilika 🥳

09/09/2026

Kapena mukufuna Ka video kampanda womwe Poetry Association of Malawi yamanga ndi chithandizo cha Copyright Fund! Say no more iwe!

Thank you Copyright Fund! Alakatuli amtsogolo adzakhale ndikofikira basi!

Ulakatuli Uvale Ulemu Mesa!

Rivermark yapanga sponsor mpikisano wa ndakatulo wa okhawo amene ali ma members a Poetry Association of Malawi. Iwo apan...
09/09/2026

Rivermark yapanga sponsor mpikisano wa ndakatulo wa okhawo amene ali ma members a Poetry Association of Malawi. Iwo apanga sponsor mpikisanowu ndi 1 Million Kwacha! Koma partner iweyo!

Tonse tikapita ku Salima kogona ndi Rivermark basi! ☺️

08/09/2026

Mawa mawali tilengeza zabwino limodzi ndi partner wathu Rivermark Lodge ya ku Salima uku!

Kogona ndi ku Rivermark. Achina Rivermark anabwera kudzatipatsa malo ogona komanso a conference apamwamba. Atichitiranso zabwino alakatuli. Khalani pompo mawa 9 O'clock mammawa!

Tikuti zatheka! Poetry Association of Malawi ndi chithandizo cha Copyright Fund tsopano yamaliza kumanga mpanda pa plot ...
08/09/2026

Tikuti zatheka! Poetry Association of Malawi ndi chithandizo cha Copyright Fund tsopano yamaliza kumanga mpanda pa plot yake mu Lilongwe!

Thank you Copyright Fund! Tsogolo lathu ndi lowala tsopano ☺️

Ulakatuli Uvale Ulemu Mesa!

Kodi iwe partner! Bwanji tilengeze zabwino lachitatuli? Bwenzi la alakatuli iwe! Chabwino tisanalengeze tiwauziretu onse...
07/09/2026

Kodi iwe partner! Bwanji tilengeze zabwino lachitatuli? Bwenzi la alakatuli iwe! Chabwino tisanalengeze tiwauziretu onse amene akunka ku Salima kuti kogona ndi ku Rivermark! Rivermark yadza!

Address

Arts House, Claim Building, P. O. Box 60402, Blantyre 6
Blantyre

Telephone

+265888853620

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Poetry Association of Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Poetry Association of Malawi:

Shortcuts

Share