Zokonda amai komanso abambo

Zokonda amai komanso abambo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Zokonda amai komanso abambo, Chiwembe P. O BOX 32, Blantyre.

2007 Nissan bluebird inbox
16/01/2024

2007 Nissan bluebird inbox

5pin basi
14/01/2024

5pin basi

13/01/2024

Zizayenda part 1

It was morning 8 o'clock pamene ndinayitanidwa ku office ya head master anandiuza k*ti ndipakile katundu wanga ndipo ndizipita chifukwa school yawo sinali ya ulere Nnawayang'ana mwa chisoni but anandikuk*tila Mano ndithu mokhudzika nnangotuluka uku ndikulira mmh 😭

Tiyambe ndi chonchi Ndine Naomi kwathu ndi ku chikwawa ndili form 2 ndimaphunzira ku mulanje makolo anga ndiwosawuka ndithu Mayi anga amalima zinthu zosiyana siyana amapanga izi k*ti azitikwanisa k*tisamalira Ndine oyamba kwathu pa ana atatu bambo anga amangokhalira kuledzera komanso akazi koma mayi anga amakonda ndithu

Pachifukwa choti bambo agulisa zipatso zonse ndalama ndikumwera mowa ndeno amayi sakwanisa kulipira sukulu fizi yanga ulendo uno. Okay let's continue nnafika ku hostel ndipo nnayamba kulira kenako nnalongeza zovala ndi ma buku anga k*ti ndikupita basi.

Next part tomorrow I'm tired 😀

Inbox
11/01/2024

Inbox

01/12/2023

Pali mkazi winawake 21 years ATI akufuna blesser ku inbox 🤣ma blesser nazoni kanyama kabwino kabwera kokha

01/11/2023

I'm in relationsleep💚

Phuma njeee 😂
Welenganiso bwino 🤣

31/10/2023

Have you been in a relationship where you feel like you are just fórcing your partner to love you 🥹😒

20/10/2023

2years osamwako fanta anthu mulungu panganipo kanthu chonde 🤦

19/10/2023

Zikomo popanga zokonda amai ndi abambo . Osat amai okha timaona k*ti amai okha okha amango tukwanana opanda kunenapo chanzelu ai . Kungonyoza ndi kunyodola anzao apamitala nao . Apa mwaganiza bwino k*t tiziuzana molakwika olo ife amuna timauzana moyenela pomwe amai ai kunyozana .

18/10/2023

Tay grin woyeee 🤣

Address

Chiwembe P. O BOX 32
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zokonda amai komanso abambo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share