Kupeza banja ndi chibwenzi Ulere

Kupeza banja ndi chibwenzi Ulere Our Target is to connect 1,000 families for free. Please if you have found what you were looking for invite your friends. Zabwino samanana.

Ngati mukufuna kuthandizidwa mwachangu komanso to save us time. Pangani izi: 1. Munena zaka zanu2. Boma lomwe muli3. Zak...
20/05/2025

Ngati mukufuna kuthandizidwa mwachangu komanso to save us time. Pangani izi:

1. Munena zaka zanu
2. Boma lomwe muli
3. Zaka za munthu yemwe mukumfuna
4. Boma lomwe munthuyo mukufuna achokere
5. Chithunzi chanu chomwe mumachidalira
6. Ngati muli NDI ana
7. Mukufuna banja kapena chibwenzi
8. Ngati mukufuna specifically wa HIV positive/ Negative

All details are confidential. And your identity will be highly hidden.

Nkhani yabwino Kwa nonse omwe mwakhala mukutumiza ma message pakatipa , ena mwathandizidwa ena simumayankhidwa chifukwa ...
18/05/2025

Nkhani yabwino Kwa nonse omwe mwakhala mukutumiza ma message pakatipa , ena mwathandizidwa ena simumayankhidwa chifukwa Chakuchuluka Kwa ma messages. Kuyambira mwezi uno mpaka Chaka chamawa aliyense ofuna banja kapena chibwezi azipezeredwa ulere. Tikutitu ulere popanda charge iliyonse. Tipezeni ku inbox mwayiwu usanathe. First come, First Serve.

Amene munalumikizidwa kale awuzeni anzanu kuti abwere osachita umbombo nawonso zisawaphonye. Amene munatumiza ma details...
30/03/2023

Amene munalumikizidwa kale awuzeni anzanu kuti abwere osachita umbombo nawonso zisawaphonye. Amene munatumiza ma details anu mpaka lero simunalumikizidwe mutumizanso request yanu. 100% privacy

Invite your friends to this page too
.

Sunday lililonse muzipangidwa connect mwa ulere kuyambira nthawi ya 8:00 am-12:00pm.My name is Patience Mwenifumbo,Kwa e...
20/03/2023

Sunday lililonse muzipangidwa connect mwa ulere kuyambira nthawi ya 8:00 am-12:00pm.

My name is Patience Mwenifumbo,

Kwa ena nonse omwe mumalipira ma K100 kuti mupezeredwe mkazi kapena mamuna ziwani kuti mtengowu wasintha sopano ndipo wafika pa K500 ndipo mupasidwa mkazi kapena mamuna mmene mwakondera. Dziwani kuti munthu yemwe mumalumikizidwa naye amakhala kuti nayenso wabwera ku inbox kuti akufuna mkazi kapena mamuna sizachilendo. Zasankheni mkazi kapena mamuna motengera ndi zaka zomwe mwakonda.

Nonse omwe mukupangidwa connect osaiwala kumatumiza za mmene mwayendera ndi kuti experience yanu inali bwanji. M***a kumatumizanso nkhani zanu zosiyanasiyana kuti zifikire anthu ochuluka ndikuphunzirapo zinthu zomwe angasate mu moyo wa tsiku ndi tsiku.

Note: sitipanga za ma sugar mummies/daddies

17/12/2022

If you need random men or women the condition is that muzalandira 10 men/women if you pay K1,000 ndikusankhapo wa serious. It is simple.

Address

Blantyre
352000

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kupeza banja ndi chibwenzi Ulere posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Kupeza banja ndi chibwenzi Ulere:

Share

Category