62 BARS

62 BARS Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from 62 BARS, L city, Mangochi.

Ace Jizzy
17/07/2026

Ace Jizzy

zochita za Sunday ku city center
17/07/2026

zochita za Sunday ku city center

04/07/2026

Big shout out to my newest top fans! Someguy-zephie Mchewa

Malawi get ready with young saka
04/07/2026

Malawi get ready with young saka

21/06/2026

With Concient India – I just got recognized as one of their top fans!

17/06/2026

Udzatenge madzi Obwata Kwambili madzi otentha kapena kuti madzi Otcha oti agaduka akuchoka pa moto kumene nde udzakathile pa dzala lakwanu ! Ndikungonena Bro Usadzayelekeze Kupanga zomwe ndakuuzazi pa dzala paja pamakhala mizimu yoipa udzaona zodabwitsa ⚰️

KAUMA TIMES
ZOCHITIKA KWA KAUMA

Awa mukuwaona apawa ndi abusa Ralph luke ndi Concient India Dzana pastor Luke anadalitsa Concient India ndi Ndalama zokw...
17/06/2026

Awa mukuwaona apawa ndi abusa Ralph luke ndi Concient India Dzana pastor Luke anadalitsa Concient India ndi Ndalama zokwana 70 Thousands munthawi Yomwe Oimbayu anali pama vuto ofunikila thandizo !

Ena Chaka chawo ndi chino ena chamawa zikungosiyana nthawi basi!

( 0889296144 ) Abusa nafe tikufunikila thandizo kamachepa nkachovala

KAUMA TIMES
ZOCHITIKA KWA KAUMA

17/06/2026

4 Days chichokeleni kwao sakubwelelaso zikumveka ngati pena Pake sizili Bwino Kwa Inu amene mukumudziwa Siveliwa Jnr com...
16/06/2026

4 Days chichokeleni kwao sakubwelelaso zikumveka ngati pena Pake sizili Bwino Kwa Inu amene mukumudziwa Siveliwa Jnr comedian waku Durben Kwa Kauma mwati zatanani kumene

KAUMA TIMES
ZOCHITIKA KWA KAUMA

12/06/2026

Ku Malawi timakhala ngati tinagwirizana kuti tose tizivutika nde wina akalemera amakhala ngati waukira 😏

Address

L City
Mangochi

Telephone

+265887754112

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when 62 BARS posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to 62 BARS:

Shortcuts

Share