Romeo Hastings Bandawe

Romeo Hastings Bandawe Romeo Hastings Bandawe is the propriator of Success Estate Agents a trusted, dully registered and certified real estate company in Malawi.

11/02/2026

Mwina mumaganiza kuti SUCCESS ESTATE AGENTS imagulitsa malo ndi nyumba za ku Liwonde kokha basi.

Dinani link imene ili m'munsiyi

https://www.facebook.com/share/1ADKP3Yp6s/

Success Properties and Real Estate Company is a registered real estate company.

We offer services such as selling and buying plots and houses, sketch map production, site planning, house planning, property management, property valuation, and leasing

29/11/2025

https://www.facebook.com/share/1DEMdxQfDf/

Success Properties and Real Estate Company is a registered real estate company.

We offer services such as selling and buying plots and houses, sketch map production, site planning, house planning, property management, property valuation, and leasing

Tikugulitsa nyumba ziwiri zomangidwa mwa makono ndi cement ndi njerwa ku Liwonde pafupi ndi Machinga Secondary school, p...
21/11/2025

Tikugulitsa nyumba ziwiri zomangidwa mwa makono ndi cement ndi njerwa ku Liwonde pafupi ndi Machinga Secondary school, plot ndi 20m by 35m, pali kware ndi njerwa komanso pali malo omanga nyumba zina, madzi analumikizidwa kale, magetsi ali pompo, pambali pa msewu.

Mtengo ndi 25 million kwacha kukambirana kulipo.

Pangani follow komanso like pa page's athu Success Estate Agents komanso Success Real Estate Company kuti mudziona malonda amalo ndi nyumba mosavuta.

0999 853 358/0888 853 358

21/11/2025

Nyumba ziwiri zogulitsa pa plot imodzi ku Liwonde pafupi ndi Machinga Secondary School, madzi analumikizidwa kale, magetsi ali pompo, palinso malo omangapo nyumba zina ziwiri, pambali pa msewu, plot 20m by 35m

Mtengo woyambira ndi 25 million kwacha kukambirana.
0999 853 358/ 0888 853 358

https://youtube.com/?si=q0asARPO9BMxBQl7
20/11/2025

https://youtube.com/?si=q0asARPO9BMxBQl7

A registered and certified real estate company based in Machinga, Malawi, that provides the general public with real estate services such as buying and selling plots and houses, estates and farms, planning and producing sketchmas, prpery valuation, property management, searching for houses and offic...

05/11/2025

0999 853 358/0888 853 358

05/11/2025

Malo ogulitsa pambali penipeni pa msewu wafumbi ku Liwonde ku roadblock, magetsi ndi madzi zili pompo, kukula kwa malo 37m by 20m

Mtengo 2.9 million kwacha.

0999 853 358/0888 853 358

04/11/2025

Malo ogulitsa abwino koma otsika mtengo ku Liwonde pafupi ndi Nankhukwa Steel Company mmsewu wopita ku Zomba 15m by 30m magetsi ndi madzi zili pafupi Mtengo 1.9 million kwacha.

0999 853 358 komanso 0888 853 358

04/11/2025

Malo ogulitsa abwino koma otsika mtengo ku Liwonde ku tsanya ena amati ku green malata, 16m by 44m pamtunda posaima madzi. Mtengo 1.2 million kwacha kukambirana kulipo. 0999 853 358 kapena 0888 853 358

04/11/2025

Malo ogulitsa abwino posaima madzi nyengo yamvula, ali m'mudzi mwa Katundu ku Mangochi turn off pafupi ndi msewu wathala ndi 15m by 25m magetsi ndi madzi zili pompo kungolumikiza msewu uliponso wa galimoto.

Mtengo ndi 2.2 million kwacha kukambirana kulipo

0999 853 358 komanso 0888 853 358

04/11/2025

Malo ogulitsa abwino koma otchipa ku Mangochi turn off mudzi mwa Mwalabu 15m by 30m mtengo ndi K850 000 plot iliyonse. Analipo maplot 4 tagulitsa awiri atsala awiri. Bwerani muzatngepo yanu, asanathe.

0999 853 358 komanso 0888 853 358

Address

P. O. Box 193
Liwonde

Opening Hours

Monday 07:30 - 18:00
Tuesday 07:30 - 18:00
Wednesday 07:30 - 18:00
Thursday 07:30 - 18:00
Friday 07:30 - 18:00
Saturday 08:00 - 18:00

Telephone

+265888853358

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Romeo Hastings Bandawe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Romeo Hastings Bandawe:

Share